Kodi Baibulo Limati Chiyani Za Chidziwitso? — Gawo 2 · Malemba a KJV okhala ndi Manambala a Strong — Bible Quiz
For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.
This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.
Proverbs 1:7 — Kuopa Yehova ndiye chiyambi cha nzeru. ________ zimanyoza nzeru ndi malangizo.
ochimwa
zipatso
Zitsiru
Proverbs 2:3 — ngati upempha kuti uzindikire zinthu inde kupempha ndi mtima wonse kuti ________ womvetsa zinthu
ukhale
chete
tanthauzo
Proverbs 19:2 — Si bwino kuti munthu akhale ________ nzeru; ndipo munthu woyenda mofulumira amaphonya njira.
wopanda
mtendere
ulemerero
John 17:3 — Tsono moyo ________ ndi uwu: Iwo akudziweni Inu, Mulungu yekhayo woona, ndi Yesu Khristu, amene Inu mwamutuma.
achifwamba
wosathawo
wophunzira
2 Corinthians 4:6 — Pakuti Mulungu amene anati, “Kuwala kuwunike kuchokera mu ________,” Iyeyo ndiye anawunikira mʼmitima mwathu kutipatsa kuwala kuti tidziwe ulemerero wa Mulungu umene ukuoneka pa nkhope ya Yesu Khristu.
malangizo
mdima
chikondi
Romans 1:28 — Ndipo popeza anaona kuti nʼchopanda ________ kumvera Mulungu, Iye anawasiya kuti atsatire maganizo achitayiko kuti achite zosayenera kuchitazo.
nzeru
zambiri
manyazi
1 Corinthians 8:1 — Tsopano za chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano: Ife tidziwa kuti tonse tili ndi chidziwitso. Komatu chidziwitso chokha chimadzitukumula, koma ________ ndicho chimapindulitsa.
chikondi
moyo
mphamvu
1 Timothy 6:20 — ________, samalitsa zimene unapatsidwa. Upewe nkhani zopanda pake zosalemekeza Mulungu ndiponso maganizo otsutsana amene amaganizidwa molakwika kuti ndi nzeru.
Makedoniya
Timoteyo
Efeso
Isaiah 11:9 — Sipadzakhala chilichonse chopweteka kapena chowononga pa ________ lopatulika la Yehova, pakuti anthu a dziko lapansi adzadzaza ndi nzeru yotha kudziwa Yehova monga momwe nyanja imadzazira ndi madzi.
phiri
mtundu
mtengo
Habakkuk 2:14 — Pakuti dziko lapansi lidzadzaza ndi chidziwitso cha ________ wa Yehova, monga momwe madzi amadzazira nyanja.
moyo
ulemerero
mphamvu
Numbers 14:21 — Komabe, ndikunenetsa kuti ________ Ine, ndiponso pamene dziko lapansi ladzaza ndi ulemerero wa Yehova
popanda
pali
zoona
Ecclesiastes 4:12 — Munthu mmodzi angathe kugonjetsedwa, koma anthu awiri akhoza kudziteteza. ________ cha maulusi atatu sichidukirapo.
Ndidzatumiza
Mlaliki
Chingwe
Hosea 6:3 — Tiyeni timudziwe Yehova, tiyeni tilimbike kumudziwa Iye. Adzabwera kwa ife mosakayikira konse ngati kutuluka kwa ________; adzabwera kwa ife ngati mvula ya mʼchilimwe, ngati mvula ya nthawi yamphukira imene imakhathamiritsa nthaka.”
phiri
khomo
dzuwa
2 Peter 3:18 — Koma kulani mu ________ ndi mʼchidziwitso cha Ambuye ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu. Kwa Iye kukhale ulemerero tsopano mpaka muyaya. Ameni.
chisomo
thupi
Wabwino
Link copied
Has this study helped you? Share a short or your full testimony — your story helps someone else find this site.
Save your progress
Optional. You never need an account to use this site.
Keep your quiz scores and your certificate if you change phone or clear your browser.
Restore progress
Restoring replaces the progress on this device, and any certificate you print afterwards will carry the name on the record.
