🌐 Language
'Olelo Hawai'iAfaan Oromoobahasa IndonesiaBelarusianBrezhonegCebuanoChamorroChichewachiShonaChongthuCiyawoDanskDeutschEestiEnglishEspañolEsperantoeʋegbeFrançaisHausaHrvatskiIgboIlocanoItalianoKikuyuKiswahiliKiyombiKreyòl AyisyenLatinaLatviešulietuviųLingálaLugandaMagyarMahasuiMāoriNederlandsNorskPohnpeianPolskiPortuguêsQach’abelRomaniRomânăSanskritSetswanaShqipsrpski jezikSuomiSvenskaTagalogTiếng ViệtTonganTwiTürkçeUyghur tiliYorùbáÍslenskaČeštinaБългарскиРусскийУкраїнськаעבריתاردوالعربيةفارسیكوردی سۆرانیअहिराणी‎नेपालीभद्रवाही‎मराठीमानक हिन्दी‎हरियाणवी‎অসমীয়াবাংলাਪੰਜਾਬੀગુજરાતીଓଡ଼ିଆ‎தமிழ்తెలుగుಕನ್ನಡമലയാളംไทยဗမာἙλληνική中文日本語한국어+ Zilankhulo zonse
See More Jesus
Chichewa

Kodi Baibulo Limanena Chiyani Za Kuopa Mulungu? — Kuchiyika M'ntchito · Malemba a KJV okhala ndi Manambala a Strong — Mafunso a Baibulo

Mafunso a Baibulo

Kodi Baibulo Limanena Chiyani Za Kuopa Mulungu? — Kuchiyika M'ntchito · Malemba a KJV okhala ndi Manambala a Strong — Mafunso a Baibulo

Pa lemba lililonse pansipa, sankhani chimene vesiyo limaphunzitsa. Zambiri zanu zidzaonekera kumapeto.

Awa ndi mayeso oyesedwa. Apambaneni kuti mupeze mfundo zopita ku Satifiketi ya Chivomerezo cha Utumiki yanu.

2 Petro 1:3 — Mulungu mwa mphamvu zake anatipatsa zonse zofunika kukhala moyo opembedza, potidziwitsa za Iyeyo amene anatiyitana ku ulemerero wake ndi ________ wake.
ubwino
kufatsa
mʼbado
1 Petro 2:2 — Monga ________ obadwa kumene amalirira mkaka, inunso muzilakalaka mkaka weniweni wauzimu, kuti mukule ndi kukufikitsani ku chipulumutso chanu
zilakolako
makanda
mipando
Hoseya 11:3 — Ndi Ine amene ndinaphunzitsa ________ kuyenda, ndipo ndinawagwira pa mkono; koma iwo sanazindikire kuti ndine amene ndinawachiritsa.
Efereimu
Asiriya
Samariya
Ahebri 11:6 — Ndipo popanda chikhulupiriro nʼkosatheka kukondweretsa Mulungu, chifukwa aliyense amene amabwera kwa Iye ayenera kukhulupirira kuti Mulungu alipodi ndi kuti Iye amapereka ________ kwa amene akumufunitsitsa.
wosatha
chisomo
mphotho
Machitidwe a Atumwi 3:2 — Ndipo munthu wolumala chibadwire ankanyamulidwa tsiku ndi tsiku kukayikidwa pa khomo la Nyumbayo lotchedwa Khomo Lokongola kuti azikapempha amene amalowa ku ________ la Nyumbayo.
chuma
bwalo
mbalame
Machitidwe a Atumwi 3:8 — Iye analumpha ndi kuyamba kuyenda. Kenaka ________ nawo pamodzi mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu, akuyenda ndi kulumpha ndiponso kuyamika Mulungu.
waufumu
banja
analowa
Genesis 5:24 — ________ anayenda ndi Mulungu; ndipo iye sanaonekenso chifukwa Mulungu anamutenga.
Hamori
Biliha
Enoki
Genesis 6:9 — Mbiri ya Nowa inali yotere: Nowa anali munthu wolungama ndi wopanda tchimo pakati pa anthu a ________ wake. Ndipo anayenda ndi Mulungu.
manyazi
chovala
mʼbado
Genesis 17:1 — Pamene ________ anali ndi zaka 99, Yehova anamuonekera nati, “Ine ndine Mulungu Wamphamvuzonse. Ukhale munthu wochita zolungama nthawi zonse.
Isake
Abimeleki
Abramu
Mika 6:8 — Munthu iwe, Yehova wakuonetsa kale chimene chili chabwino. Tsono kodi Yehova akuyembekezera chiyani kwa iwe? Uzichita zolungama ndi kukonda ________ ndiponso kuyenda modzichepetsa pamaso pa Mulungu wako.
chifundo
machimo
banja
Masalimo 4:3 — Dziwani kuti Yehova wadziyikira ________ anthu okhulupirika; Yehova adzamva pamene ndidzamuyitana.
padera
muvi
mana
Akolose 1:10 — Ndipo tikupempherera zimenezi ndi cholinga chakuti inu mukhale moyo oyenera Ambuye ndi kumukondweretsa mʼnjira zonse. Kubereka chipatso pa ntchito iliyonse ________, ndi kukula mʼchidziwitso cha Mulungu.
yabwino
mwamphamvu
okondedwa
1 Yohane 2:6 — Aliyense amene amati ________ mwa Mulungu, ayenera kukhala moyo umene Yesu ankakhala.
amachita
chake
amakhala
1 Timoteyo 2:1 — Tsono choyamba ndikukupemphani kuti mupempherere anthu onse. ________ anu akhale opemba, opempha, opempherera ena ndi oyamika.
ziwalo
zozizwitsa
Mapemphero
1 Timoteyo 6:6 — Koma ________ Mulungu kuli ndi phindu lalikulu.
kulemekeza
kupitiriza
kunyoza
Tito 2:12 — Chisomo chimatiphunzitsa kukana moyo osalemekeza Mulungu komanso ________ za dziko lapansi. Ndipo chimatiphunzitsa kukhala moyo odziletsa, olungama ndi opembedza Mulungu nthawi ino
makanda
zilakolako
nkhunda
1 Timoteyo 6:11 — Koma iwe, munthu wa Mulungu, thawa zinthu zonsezi. Tsatira chilungamo, moyo wolemekeza Mulungu, chikhulupiriro, chikondi, kupirira ndi ________.
kufatsa
mʼmayesero
chikhululukiro
1 Timoteyo 6:12 — Menya nkhondo yabwino yachikhulupiriro. Gwiritsitsa moyo ________ umene anakuyitanira pamene unavomereza bwino lomwe pamaso pa mboni zambiri.
utumiki
wosatha
Malemba
1 Timoteyo 1:18 — Mwana wanga ________, ndikukupatsa langizo ili molingana ndi maulosi amene aneneri ananena za iwe. Pamene ukumbukira mawu amenewa udzatha kumenya bwino nkhondo
Makedoniya
Kaisara
Timoteyo
2 Timoteyo 2:3 — Umve nane zowawa, monga ________ wa Khristu Yesu.
msilikali
chisomo
utumiki
2 Timoteyo 2:4 — Palibe msilikali amene ali pa ntchito amagwiranso ntchito za anthu wamba, iye amafuna ________ bwana wolamulira.
kulemekeza
kukondweretsa
kupitiriza
Aefeso 6:11 — Valani zida zonse za Mulungu kuti muthe kuyima ndi kukana machenjerero a ________.
Satana
Nowa
Paulo
2 Timoteyo 3:12 — ________ zoona, munthu aliyense amene akufuna kukhala moyo wolemekeza Mulungu mwa Khristu Yesu, adzazunzikadi
gawo
mtendere
Kunena
1 Akorinto 9:24 — Kodi simukudziwa kuti pa mpikisano wa liwiro onse amathamanga ndithu, koma mmodzi ________ ndiye amalandira mphotho? Motero thamangani kuti mupate mphotho.
Uthenga
mphamvu
yekha
1 Akorinto 9:25 — Aliyense wochita mpikisano amakonzekera mwamphamvu. ________ izi kuti alandire mphotho yankhata yamaluwa yomwe imafota. Koma ife timachita izi kuti tilandire mphotho yosafota.
amakhala
Amachita
udzu
Ahebri 12:1 — Tsono popeza ifenso tazunguliridwa ndi gulu lalikulu la mboni, tiyeni titaye chilichonse chimene chimatitchinga, ________ tchimo limene limatikola mosavuta, ndipo tithamange ndi khama mpikisano umene tayambawu.
makamaka
mwamphamvu
okondedwa
Yesaya 40:31 — koma iwo amene ________ Yehova adzalandira mphamvu zatsopano. Adzawuluka ngati chiwombankhanga; adzathamanga koma sadzalefuka, adzayenda koma sadzatopa konse.
amakondwera
akulamulira
amakhulupirira
1 Timoteyo 4:8 — Pakuti kulimbitsa ________ kumapindulitsapo pangʼono, koma moyo woopa Mulungu umapindulitsa pa zonse. Umatilonjeza moyo pa moyo uno ndiponso pa moyo umene ukubwerawo.
chisomo
thupi
yekha
2 Timoteyo 4:7 — Ndamenya nkhondo ________, ndatsiriza bwino mpikisano wa liwiro ndipo ndasunga chikhulupiriro.
makamaka
yabwino
mwamphamvu

← Bwererani ku phunziroli