Kodi Baibulo Limati Chiyani Pankhani ya Kuleza Mtima? — Gawo 2 · Malemba a KJV ndi Manambala a Strong's — Bible Quiz
For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.
This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.
Ahebri 10:36 — Nʼkofunika kuti mupirire kuti pamene muchita chifuniro cha Mulungu mudzalandire zimene Iye ________.
anazindikira
mdulidwe
analonjeza
Ahebri 12:1 — Tsono popeza ifenso tazunguliridwa ndi gulu lalikulu la mboni, tiyeni titaye chilichonse chimene chimatitchinga, ________ tchimo limene limatikola mosavuta, ndipo tithamange ndi khama mpikisano umene tayambawu.
makamaka
okondedwa
mwamphamvu
Ahebri 6:15 — Ndipo Abrahamu atayembekezera ________, analandira zimene anamulonjezazo.
Potsiriza
makamaka
mofatsa
Yakobo 5:7 — Tsono abale, pirirani mpaka kubwera kwa Ambuye. Onani mmene amachitira mlimi. Amadikirira kuti ________ zabwino zioneke mʼmunda mwake. Amayembekezera mokhazikika mtima kuyambira nthawi ya mvula yoyamba mpaka yotsiriza.
chisomo
chuma
zipatso
Yakobo 5:11 — Monga mukudziwa, tinawatenga ngati odalitsika anthu amene anapirira. Munamva za kupirira kwa ________ ndipo mwaona zimene Ambuye anamuchitira potsiriza pake. Ambuye ndi wodzaza ndi chisoni ndi chifundo.
Aramu
Yese
Yobu
Aroma 15:4 — Pakuti zilizonse zimene zinalembedwa kale zinalembedwa kuti zitiphunzitse ife. Malembawo amatilimbikitsa kupirira kuti tikhale ndi ________.
thupi
chiyembekezo
wolungama
Aroma 15:5 — Mulungu amene amapereka kupirira ndi chilimbikitso akupatseni ________ amodzi pakati panu monga inu mukutsatira Khristu Yesu
maganizo
magulu
mizinda
Akolose 1:11 — Timapempheranso kuti Mulungu akulimbikitseni ndi mphamvu yake yonse ya ulemerero wake, kuti muzipirira zonse ndi mitima yofatsa ndi ya ________
chete
chimwemwe
umboni
Masalimo 37:7 — Khala ________ pamaso pa Yehova ndipo umudikire mofatsa; usavutike pamene anthu apambana mʼnjira zawo, pamene iwo achita zinthu zawo zoyipa.
chimwemwe
mavuto
chete
Masalimo 40:1 — ________ ndinadikira Yehova Iye anatembenukira kwa ine ndipo anamva kulira kwanga.
Mofatsa
mwamphamvu
zokoma
Maliro 3:26 — nʼkwabwino kudikira ________ cha Yehova modekha.
chimwemwe
chipulumutso
chete
Yobu 13:15 — Ngakhale Iye andiphe, komabe ndidzamukhulupirira; ndithu, ndidzafotokoza ________ wanga pamaso pake.
mwala
mlandu
anatsogolera
2 Atesalonika 3:5 — Ambuye atsogolere ________ yanu kuti mudziwe chikondi cha Mulungu ndiponso kupirira kumene Khristu amapereka.
Woyera
mwamuna
mitima
Yakobo 1:12 — Wodala ndi munthu amene amapirira ________, chifukwa akapambana adzalandira chipewa cha ulemerero chimene Mulungu analonjeza anthu amene amamukonda.
chikhululukiro
kufatsa
mʼmayesero
Link copied
Has this study helped you? Share a short or your full testimony — your story helps someone else find this site.
Save your progress
Optional. You never need an account to use this site.
Keep your quiz scores and your certificate if you change phone or clear your browser.
Restore progress
Restoring replaces the progress on this device, and any certificate you print afterwards will carry the name on the record.
