🌐 Language
'Olelo Hawai'iAfaan Oromoobahasa IndonesiaBelarusianBrezhonegCebuanoChamorroChichewachiShonaChongthuCiyawoDanskDeutschEestiEnglishEspañolEsperantoeʋegbeFrançaisHausaHrvatskiIgboIlocanoItalianoKikuyuKiswahiliKiyombiKreyòl AyisyenLatinaLatviešulietuviųLingálaLugandaMagyarMahasuiMāoriNederlandsNorskPohnpeianPolskiPortuguêsQach’abelRomaniRomânăSanskritSetswanaShqipsrpski jezikSuomiSvenskaTagalogTiếng ViệtTonganTwiTürkçeUyghur tiliYorùbáÍslenskaČeštinaБългарскиРусскийУкраїнськаעבריתاردوالعربيةفارسیكوردی سۆرانیअहिराणी‎नेपालीभद्रवाही‎मराठीमानक हिन्दी‎हरियाणवी‎অসমীয়াবাংলাਪੰਜਾਬੀગુજરાતીଓଡ଼ିଆ‎தமிழ்తెలుగుಕನ್ನಡമലയാളംไทยဗမာἙλληνική中文日本語한국어+ All languages
See More Jesus

Kodi Baibulo Limati Chiyani Za Nzeru? — Maziko · Malemba a KJV Ndi Manambala a Strong's — Bible Quiz

For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.

This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.

Psalm 111:10 — Kuopa Yehova ndicho chiyambi cha nzeru; onse amene amatsatira ________ ake amamvetsa bwino zinthu. Iye ndi wotamandika mpaka muyaya.
malangizo
kumene
njira
Proverbs 2:7 — Anthu olungama zinthu zimawayendera bwino chifukwa Yehova amakhala nawo. Paja Yehova ndiye ________ cha amene amayenda mwangwiro
pafupifupi
chishango
matemberero
Proverbs 2:4 — ngati ufunafuna nzeruyo ngati ________ ndi kuyisakasaka ngati chuma chobisika
siliva
vinyo
ulemu
Ecclesiastes 12:13 — Basi zonse zamveka; mathero a nkhaniyi ndi awa: uziopa Mulungu ndi kusunga ________ ake, pakuti umenewu ndiwo udindo wa anthu onse.
malangizo
nkhosa
malamulo
Psalm 34:9 — Wopani Yehova inu ________ mtima ake, pakuti iwo amene amaopa Iye sasowa kanthu.
oyera
malangizo
mibado
Psalm 103:11 — Pakuti monga ________ kuli kutali ndi dziko lapansi, koteronso chikondi chake nʼchachikulu kwa iwo amene amamuopa;
nyanja
kumwamba
moto
Proverbs 8:13 — Kuopa Yehova ndiko kudana ndi zoyipa. Ine ndimadana ndi ________, kudzitama, kuchita zoyipa, ndiponso kuyankhula zonyenga.
Mayendedwe
zosungiramo
kunyada
Proverbs 16:6 — Chifukwa cha chikondi chosasinthika ndi kukhulupirika, munthu amakhululukidwa ________ ake; chifukwa cha kuopa Yehova munthu amapewa zoyipa.
nsalu
ulemerero
machimo
Proverbs 19:23 — Kuopa Yehova kumabweretsa ________; wotereyo amakhala mu mtendere; ndiye kuti choyipa sichidzamugwera.
moyo
bwino
wantchito
Acts 9:31 — Pamenepo mpingo wa ku ________ konse, ku Galileya ndi ku Samariya unakhala pamtendere, unalimbikitsidwa; ndi kupatsidwa mphamvu ndi Mzimu Woyera, unakula mʼchiwerengero, ndi kukhala moopa Ambuye.
Yudeya
Asiya
Damasiko
2 Corinthians 7:1 — Abwenzi okondedwa, popeza tili ndi ________ amenewa, tiyeni tidziyeretse, kusiyana nazo zilizonse zimene zikhoza kudetsa thupi ndi mzimu, ndipo tiyesetse kukhala oyera mtima poopa Mulungu.
zilakolako
mayesero
malonjezo
Philippians 2:12 — Tsono, ________ anga okondedwa, monga mwakhala omvera nthawi zonse, osati pamene ndinali nanu pokha, koma tsopano koposa pamene ndili kutali. Pitirizani kugwira ntchito ya chipulumutso chanu mwa mantha ndi kunjenjemera
mdulidwe
chikondi
abwenzi

← Back to the study