Kodi Baibulo Limanena Chiyani Za Chidziwitso? — Maziko · Malemba a KJV okhala ndi Manambala a Strong — Bible Quiz
For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.
This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.
Proverbs 11:9 — Munthu ________ amawononga mnansi wake ndi pakamwa pake, koma munthu wolungama amapulumuka chifukwa cha kudziwa zinthu.
chambiko
chishango
wosapembedza
Proverbs 12:1 — Munthu amene amakonda mwambo amakonda kudziwa zinthu, koma amene amadana ndi ________ ndi wopusa.
chidzudzulo
bwenzi
kunyada
Proverbs 15:14 — Mtima wa munthu wozindikira zinthu umafunafuna nzeru, koma pakamwa pa zitsiru pamadya ________ wawo.
kukhulupirika
uchitsiru
tanthauzo
Proverbs 24:5 — Munthu wodziwa zinthu ali ndi mphamvu yayikulu kuposa munthu wanyonga ________, ndipo munthu wachidziwitso amaposa munthu wamphamvu.
chilango
zambiri
wowukira
Isaiah 5:13 — Motero anthu anga adzatengedwa ________ chifukwa cha kusamvetsa zinthu; atsogoleri awo olemekezeka adzafa ndi njala, ndipo anthu wamba ochuluka adzafa ndi ludzu.
ukapolo
malangizo
mʼchipululu
Luke 4:18 — “Mzimu wa Ambuye ali pa Ine; chifukwa wandidzoza kuti ndilalikire Uthenga Wabwino kwa osauka. Wandituma kuti ndilalikire kwa a ________ kuti amasulidwe ndi kwa osaona kuti apenyenso, kumasulidwa kwa osautsidwa
umboni
mʼndende
mbalame
2 Timothy 2:25 — Otsutsana naye awalangize ________, mwina Mulungu adzawapatsa mwayi woti asinthike ndi kuzindikira choonadi.
molondola
mofatsa
momveka
Isaiah 28:9 — Iwo akuti, “Kodi munthu ameneyu akufuna aphunzitse ndani? Uthengawu akufuna kufotokozera yani? Ndi kwa ana amene aleka kuyamwa, kwa ________ ongowachotsa kumene ku bere?
mitumbira
makanda
mikungudza
1 Corinthians 3:1 — Ndipo abale sindikanakuyankhulani ngati auzimu koma adziko lapansi, ________ chabe mwa Khristu.
makanda
mayesero
anamwali
1 Corinthians 3:2 — Ndinakupatsani mkaka osati ________ cholimba pakuti munali musanakonzeke kuchilandira. Zoonadi, simunakonzekebe.
chakudya
Wabwino
Ngakhale
Hebrews 5:14 — Koma chakudya cholimba ndi cha anthu okhwima msinkhu, amene pogwiritsa ntchito nzeru zawo, aphunzira ________ chabwino ndi choyipa.
kusiyanitsa
utumiki
pafupifupi
Isaiah 40:13 — Ndani anapereka ________ kwa Mzimu wa Yehova kapena kumuphunzitsa Iye monga phungu wake?
kumene
njira
malangizo
Romans 10:2 — Popeza ndiwachitira ________ kuti ndi achangu pa zinthu za Mulungu koma osati mwachidziwitso.
wolungama
ukapolo
umboni
2 Peter 3:18 — Koma kulani mu ________ ndi mʼchidziwitso cha Ambuye ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu. Kwa Iye kukhale ulemerero tsopano mpaka muyaya. Ameni.
chisomo
Wabwino
chuma
Link copied
Has this study helped you? Share a short or your full testimony — your story helps someone else find this site.
Save your progress
Optional. You never need an account to use this site.
Keep your quiz scores and your certificate if you change phone or clear your browser.
Restore progress
Restoring replaces the progress on this device, and any certificate you print afterwards will carry the name on the record.
