Ndiyenera Kuchita Chiyani Kuti Ndipulumutsidwe? — Gawo 2 · Malemba a KJV pamodzi ndi Manambala a Strong — Bible Quiz
For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.
This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.
Matthew 16:24 — Pamenepo Yesu anati kwa ophunzira ake, “Ngati wina aliyense abwera pambuyo panga ayenera kudzikana ndi kutenga ________ wake ndi kunditsata Ine.
wamphesa
mbiri
mtanda
Luke 9:23 — Ndipo Iye anawuza onse kuti, “Ngati wina aliyense akufuna kutsata Ine, ayenera kudzikana yekha ndi kusenza ________ wake tsiku ndi tsiku nʼkumanditsata Ine.
chiphunzitso
mtanda
wamphesa
Lamentations 3:22 — Ife sitinawonongekeretu chifukwa chikondi cha Yehova ndi chachikulu, ndi ________ chake ndi chosatha.
machimo
mdani
chifundo
Proverbs 8:34 — Wodala munthu amene amandimvera, amene amakhala pa ________ panga tsiku ndi tsiku, kudikirira pa chitseko changa.
malire
khomo
ndodo
Acts 17:11 — Tsopano anthu a ku Bereya anali akhalidwe labwino kusiyana ndi Atesalonika, pakuti iwo analandira mawu ndi chidwi chachikulu ndipo ankasanthula ________ tsiku ndi tsiku kuti aone ngati zimene ankanena Paulozo zinali zoona.
mizimu
Malemba
zinayi
Matthew 6:9 — “Chifukwa chake pempherani motere: “‘________ athu akumwamba, dzina lanu lilemekezedwe
Atate
wantchito
Khristu
Psalm 68:19 — Matamando akhale kwa Ambuye, kwa Mulungu ________ wathu amene tsiku ndi tsiku amasenza zolemetsa zathu.
Mpulumutsi
Aamori
Wamphamvuzonse
Romans 8:16 — Mzimu ________ amavomerezana ndi mzimu wathu kuti ife ndife ana a Mulungu.
chimwemwe
manyazi
mwini
Romans 8:26 — Momwemonso, Mzimu amatithandiza ife mʼkufowoka kwathu. Ife sitidziwa momwe tiyenera kupempherera koma Mzimu ________ amatipempherera mobuwula ndi mawu osafotokozedwa.
chimwemwe
mwini
manyazi
Galatians 5:16 — Choncho ine ndikuti, mulole kuti Mzimu akutsogolereni ndipo simudzachita zofuna za ________ lanu la uchimo.
Wabwino
thupi
chisomo
Galatians 5:22 — Koma chipatso cha Mzimu Woyera ndi chikondi, chimwemwe, mtendere, kuleza mtima, chifundo, kukoma mtima, ________
abwenzi
kuuka
kukhulupirika
Philippians 2:12 — Tsono, abwenzi anga okondedwa, monga mwakhala omvera nthawi zonse, osati pamene ndinali nanu pokha, koma tsopano koposa pamene ndili kutali. Pitirizani kugwira ntchito ya ________ chanu mwa mantha ndi kunjenjemera
mdulidwe
chipulumutso
chete
Jude 1:20 — Koma inu okondedwa, muthandizane kuti mukule pa ________ chanu choyera, ndipo muzipemphera ndi mphamvu ya Mzimu Woyera.
chikhulupiriro
mtendere
zipatso
Acts 2:39 — Pakuti lonjezoli ndi lanu ndi ana anu ndiponso la onse amene ali ________, ndi iwo onse amene Ambuye Mulungu wathu adzawayitane.”
kutali
chimwemwe
kuwala
Joel 2:28 — “Ndipo patapita nthawi, ndidzakhuthulira Mzimu wanga pa anthu onse. Ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzanenera, nkhalamba zanu zidzalota maloto, anyamata anu adzaona ________.
otsala
masomphenya
bwanamkubwa
Joshua 24:15 — Koma ngati kutumikira Yehova kukuyipirani, sankhani lero amene mudzamutumikire, kapena milungu imene makolo anu ankayitumikira kutsidya kwa mtsinje wa ________, kapena milungu ya Aamori, amene mukukhala mʼdziko lawo. Koma ine ndi banja langa, tidzatumikira Yehova.”
Yufurate
Mizipa
Seiri
2 Timothy 1:5 — Ndakumbukira za ________ chako choona chimene chinayamba mwa agogo ako a Loisi ndi mwa amayi ako Yunike ndipo ndikutsimikiza mtima kuti chilinso mwa iwe.
mphamvu
chisomo
chikhulupiriro
Deuteronomy 7:9 — Choncho dziwani kuti Yehova Mulungu wanu, ndi Mulungu. Iye ndi Mulungu wokhulupirika, wosunga ________ lake la chikondi chosasinthika ku mibadomibado, kwa iwo amene amamukonda nasunga malamulo ake.
mphamvu
pangano
mwamuna
Exodus 16:21 — ________ uliwonse aliyense amatola zimene amazifuna, ndipo dzuwa likatentha zimasungunuka.
pamwamba
Mmawa
guwa
Link copied
Has this study helped you? Share a short or your full testimony — your story helps someone else find this site.
Save your progress
Optional. You never need an account to use this site.
Keep your quiz scores and your certificate if you change phone or clear your browser.
Restore progress
Restoring replaces the progress on this device, and any certificate you print afterwards will carry the name on the record.
