Kodi Baibulo Limanena Chiyani Za Nzeru? — Kuyichita M'moyo · Malemba a KJV pamodzi ndi Manambala a Strong's — Bible Quiz
For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.
This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.
Yakobo 1:5 — Ngati wina pakati panu akusowa nzeru, apemphe kwa Mulungu amene ________ kwa onse mwaulere ndi mosatonzera, ndipo adzapatsidwa.
amadziwa
amapereka
amachita
Miyambo 2:3 — ngati upempha kuti uzindikire zinthu inde kupempha ndi mtima wonse kuti ________ womvetsa zinthu
ukhale
chete
ukali
Miyambo 2:4 — ngati ufunafuna nzeruyo ngati ________ ndi kuyisakasaka ngati chuma chobisika
siliva
ulemu
vinyo
Miyambo 2:6 — Pakuti Yehova ndiye amapereka nzeru, ndipo mʼkamwa mwake mumachokera ________ ndi kumvetsa zinthu.
mphotho
chidziwitso
zipatso
Miyambo 1:7 — Kuopa Yehova ndiye chiyambi cha nzeru. ________ zimanyoza nzeru ndi malangizo.
ochimwa
malamulo
Zitsiru
Miyambo 9:10 — Kuopa Yehova ndiye chiyambi cha nzeru; ________ Woyerayo ndiko kukhala womvetsa bwino zinthu.
kudziwa
uchi
tulo
Yobu 28:28 — Ndipo Iye anati kwa munthu, ‘Taonani, kuopa Ambuye, ndiye nzeru zimenezo ndipo kuthawa ________ ndiye kumvetsa zinthu kumeneko.’”
lupanga
nyanja
zoyipa
Miyambo 4:7 — Fundo yayikulu pa za nzeru ndi iyi: upeze nzeru. Kaya ________ china chilichonse chimene ungapeze, koma upeze nzeru yomvetsa bwino zinthu.
pali
yabwino
popanda
Mateyu 7:7 — “Pemphani ndipo mudzapatsidwa; funafunani ndipo mudzapeza; ________ ndipo adzakutsekulirani.
kuchenjera
gogodani
bata
Miyambo 4:8 — Uyilemekeze nzeruyo ndipo idzakukweza; ikumbatire nzeruyo ndipo idzakupatsa ________.
ulemu
chuma
vinyo
Miyambo 3:22 — Zimenezi zidzakupatsa moyo, moyo wake wosangalatsa ndi wabwino ngati mkanda wa ________.
wochimwa
chitetezo
mʼkhosi
Masalimo 90:12 — Tiphunzitseni kuwerenga masiku athu ________, kuti tikhale ndi mtima wanzeru.
molondola
momveka
mofatsa
Deuteronomo 4:6 — Muwasunge mosamalitsa pakuti zimenezi zidzaonetsa nzeru zanu ndi kuzindikira kwanu kwa anthu a mitundu ina, amene adzamva za ________ onsewa nati, “Ndithudi, mtundu waukulu uwu ndi wa anthu anzeru ndi ozindikira.”
njira
malangizo
nkhosa
Akolose 4:5 — ________ anu pakati pa akunja, akhale anzeru ndipo mugwiritse ntchito mpata uliwonse umene muli nawo.
osankhidwa
wantchito
Mayendedwe
Aefeso 5:15 — Samalani ________ anu, musakhale ngati opanda nzeru koma ngati anzeru.
ubatizo
chinsinsi
makhalidwe
Mlaliki 9:14 — Panali mzinda waungʼono umene unali ndi anthu owerengeka. Ndipo mfumu yamphamvu inabwera kudzawuthira ________, inawuzungulira ndi kumanga mitumbira yankhondo.
miyala
kuwonongedwa
nkhondo
Mlaliki 9:15 — Tsono mu mzindamo munali munthu wosauka koma wanzeru, ndipo anapulumutsa mzindawo ndi nzeru zakezo. Koma palibe amene ________ munthu wosaukayo.
anakumbukira
anatsogolera
kunyozedwa
Miyambo 24:5 — Munthu wodziwa zinthu ali ndi mphamvu yayikulu ________ munthu wanyonga zambiri, ndipo munthu wachidziwitso amaposa munthu wamphamvu.
chilungamo
kuposa
ulemu
Miyambo 21:22 — Munthu wanzeru amagonjetsa mzinda wa anthu amphamvu ndi kugwetsa ________ limene iwo amalidalira.
kukongola
malonda
linga
Aefeso 6:17 — Valani ________ cha chipulumutso ndi kutenga lupanga la mzimu, limene ndi Mawu a Mulungu.
chipewa
zauzimu
ubatizo
Luka 21:15 — Pakuti Ine ndidzakupatsani mawu ndi nzeru kotero kuti palibe mmodzi wa ________ anu adzathe kuwakana kapena kuwatsutsa.
mbuye
adani
makolo
2 Timoteyo 3:15 — Kuyambira uli wamngʼono wakhala ukudziwa ________ Oyera, amene akhoza kukupatsa nzeru zokupulumutsa kudzera mʼchikhulupiriro cha mwa Yesu Khristu.
Malemba
wosatha
umboni
Mateyu 10:16 — “Taonani ndikukutumizani inu monga nkhosa pakati pa ________. Chifukwa chake khalani ochenjera ngati njoka ndi woona mtima ngati nkhunda.
ngale
chinsalu
mimbulu
Yakobo 3:15 — “Nzeru” zotere sizochokera kumwamba koma ndi za mʼdziko lapansi, si zauzimu koma ndi za ________.
ziwanda
amasiye
ochimwa
Yakobo 3:17 — Koma nzeru imene imachoka kumwamba, poyamba ndi yangwiro, ndi yokonda mtendere, yoganizira za ena, yogonjera, yodzaza ndi ________ ndi chipatso chabwino, yosakondera ndi yoona mtima.
pemphero
chifundo
bwenzi
1 Akorinto 1:24 — Koma kwa iwo amene Mulungu anawayitana, Ayuda ndi ________ omwe, Khristu ndi mphamvu ya Mulungu ndi nzeru za Mulungu.
Aanaki
Myuda
Agriki
1 Akorinto 1:30 — Nʼchifukwa cha Iye kuti inu muli mwa Khristu Yesu, amene wakhala nzeru ya kwa Mulungu, kwa ife, kunena kuti kulungama kwathu, chiyero ndi ________.
malangizo
chilungamo
chipulumutso
Akolose 2:3 — Mwa Iyeyu muli chuma chonse chobisidwa cha nzeru ndi ________.
kuyambira
chidziwitso
chisomo
1 Akorinto 2:7 — Ayi, ife timayankhula za nzeru yobisika ya Mulungu, nzeru imene inabisidwa ndipo imene Mulungu anatikonzera mu ________ wathu isanayambe nthawi.
manyazi
mutu
ulemerero
Link copied
Has this study helped you? Share a short or your full testimony — your story helps someone else find this site.
Save your progress
Optional. You never need an account to use this site.
Keep your quiz scores and your certificate if you change phone or clear your browser.
Restore progress
Restoring replaces the progress on this device, and any certificate you print afterwards will carry the name on the record.
