🌐 Language
'Olelo Hawai'iAfaan Oromoobahasa IndonesiaBelarusianBrezhonegCebuanoChamorroChichewachiShonaChongthuCiyawoDanskDeutschEestiEnglishEspañolEsperantoeʋegbeFrançaisHausaHrvatskiIgboIlocanoItalianoKikuyuKiswahiliKiyombiKreyòl AyisyenLatinaLatviešulietuviųLingálaLugandaMagyarMahasuiMāoriNederlandsNorskPohnpeianPolskiPortuguêsQach’abelRomaniRomânăSanskritSetswanaShqipsrpski jezikSuomiSvenskaTagalogTiếng ViệtTonganTwiTürkçeUyghur tiliYorùbáÍslenskaČeštinaБългарскиРусскийУкраїнськаעבריתاردوالعربيةفارسیكوردی سۆرانیअहिराणी‎नेपालीभद्रवाही‎मराठीमानक हिन्दी‎हरियाणवी‎অসমীয়াবাংলাਪੰਜਾਬੀગુજરાતીଓଡ଼ିଆ‎தமிழ்తెలుగుಕನ್ನಡമലയാളംไทยဗမာἙλληνική中文日本語한국어+ All languages
See More Jesus

Baibulo Limati Chiyani Za Chidziwitso? — Kuchichita M'moyo · Malemba a KJV okhala ndi Manambala a Strong — Bible Quiz

For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.

This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.

Proverbs 1:7 — Kuopa Yehova ndiye chiyambi cha nzeru. Zitsiru zimanyoza nzeru ndi ________.
tanthauzo
ukhale
malangizo
Proverbs 2:3 — ngati upempha kuti uzindikire zinthu inde kupempha ndi mtima wonse kuti ________ womvetsa zinthu
ukhale
chete
tanthauzo
Proverbs 2:4 — ngati ufunafuna nzeruyo ngati ________ ndi kuyisakasaka ngati chuma chobisika
siliva
vinyo
ulemu
Psalm 94:10 — Kodi Iye amene amalangiza ________ ya anthu sangathenso kulanga? Kodi Iye amene amaphunzitsa munthu angasowe nzeru?
nsembe
mitundu
phiri
Hosea 6:3 — Tiyeni timudziwe Yehova, tiyeni tilimbike kumudziwa Iye. Adzabwera kwa ife mosakayikira konse ngati kutuluka kwa ________; adzabwera kwa ife ngati mvula ya mʼchilimwe, ngati mvula ya nthawi yamphukira imene imakhathamiritsa nthaka.”
phiri
khomo
dzuwa
John 7:17 — Ngati munthu asankha kuchita chifuniro cha Mulungu, adzazindikira ngati ________ changa nʼchochokera kwa Mulungu kapena ngati ndi mwa Ine ndekha.
mlongo
bwenzi
chiphunzitso
Matthew 11:29 — Senzani ________ langa ndipo phunzirani kwa Ine, pakuti ndine wofatsa ndi wodzichepetsa. Ndipo inu mudzapeza mpumulo wa miyoyo yanu.
pemphero
goli
mlongo
2 Peter 3:18 — Koma kulani mu ________ ndi mʼchidziwitso cha Ambuye ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu. Kwa Iye kukhale ulemerero tsopano mpaka muyaya. Ameni.
chisomo
Wabwino
chiyembekezo
2 Peter 1:5 — Choncho, chitani khama kuwonjezera moyo wabwino pa ________ chanu, ndipo pa moyo wabwino muwonjezerepo nzeru.
chikhulupiriro
chisomo
chuma
Proverbs 15:14 — Mtima wa munthu wozindikira zinthu umafunafuna ________, koma pakamwa pa zitsiru pamadya uchitsiru wawo.
nzeru
chuma
chakudya
Colossians 1:10 — Ndipo tikupempherera zimenezi ndi cholinga chakuti inu mukhale moyo oyenera Ambuye ndi kumukondweretsa mʼnjira zonse. Kubereka chipatso pa ntchito iliyonse ________, ndi kukula mʼchidziwitso cha Mulungu.
yabwino
okondedwa
momveka
Philippians 1:9 — Ndipo ________ langa ndi lakuti chikondi chanu chipitirire kukulirakulira pa chidziwitso ndi kuzama mʼmaganizo
goli
bwenzi
pemphero
1 Corinthians 8:1 — Tsopano za chakudya choperekedwa nsembe kwa ________: Ife tidziwa kuti tonse tili ndi chidziwitso. Komatu chidziwitso chokha chimadzitukumula, koma chikondi ndicho chimapindulitsa.
malamulo
malangizo
mafano
Proverbs 3:6 — Pa zochita zako zonse uvomereze kuti Mulungu alipo, ndipo Iye adzawongola ________ zako.
malangizo
nkhosa
njira
Psalm 119:66 — Phunzitseni nzeru ndi chiweruzo chabwino, pakuti ndimakhulupirira ________ anu.
malamulo
njira
malangizo
Proverbs 24:5 — Munthu wodziwa zinthu ali ndi mphamvu yayikulu kuposa munthu wanyonga ________, ndipo munthu wachidziwitso amaposa munthu wamphamvu.
chilango
zambiri
wowukira
2 Corinthians 10:5 — Timagonjetsa ________ onse onyenga ndiponso kudzikuza kulikonse kolimbana ndi anthu kuti asadziwe Mulungu. Ndipo timagonjetsa ganizo lililonse kuti limvere Khristu.
nkhondo
maganizo
magulu
2 Corinthians 4:6 — Pakuti Mulungu amene anati, “Kuwala kuwunike kuchokera mu ________,” Iyeyo ndiye anawunikira mʼmitima mwathu kutipatsa kuwala kuti tidziwe ulemerero wa Mulungu umene ukuoneka pa nkhope ya Yesu Khristu.
malangizo
mdima
chilungamo
Ephesians 6:17 — Valani ________ cha chipulumutso ndi kutenga lupanga la mzimu, limene ndi Mawu a Mulungu.
chipewa
ubatizo
kuyambira
Malachi 2:7 — “Pakuti wansembe ayenera kukhala ndi chidziwitso, ndipo anthu ayenera kufunafuna malangizo kuchokera kwa iye, popeza iye ndi mthenga wa Yehova ________.
Wamphamvuzonse
nsembe
nyama
Proverbs 15:2 — Munthu wanzeru amayankhula zinthu za nzeru, koma pakamwa pa ________ pamatulutsa za uchitsiru.
malamulo
ochimwa
zitsiru
1 Peter 3:15 — Koma lemekezani Khristu mʼmitima mwanu ngati Ambuye wanu. Khalani okonzeka nthawi zonse kuyankha aliyense amene akufunsani za ________ chimene muli nacho.
chisomo
chiyembekezo
ulemu
2 Timothy 2:15 — Uyesetse kukhala wovomerezeka pamaso pa Mulungu monga wantchito ________ chifukwa chochitira manyazi amene amalalikira mawu achoonadi molondola.
wopanda
mtendere
ndalama
Daniel 11:32 — Ndi mawu oshashalika mfumuyo idzakopa amene anaphwanya ________, koma anthu amene amadziwa Mulungu wawo adzalimbika ndipo adzayikana mfumuyo kwathunthu.
pangano
mtumiki
mbuye
2 Timothy 2:25 — Otsutsana naye awalangize mofatsa, ________ Mulungu adzawapatsa mwayi woti asinthike ndi kuzindikira choonadi.
mwina
umboni
kuyambira
1 Corinthians 9:26 — Choncho sindithamanga monga wothamanga ________ cholinga; komanso sindichita mpikisano wankhonya monga munthu amene amangomenya mophonya.
ulemerero
wopanda
mtendere
Isaiah 11:9 — Sipadzakhala chilichonse chopweteka kapena chowononga pa ________ lopatulika la Yehova, pakuti anthu a dziko lapansi adzadzaza ndi nzeru yotha kudziwa Yehova monga momwe nyanja imadzazira ndi madzi.
phiri
mtundu
mtengo
Jeremiah 31:34 — Sipadzafunikanso kuti wina aphunzitse ________, kapena munthu wina kuphunzitsa mʼbale wake, kunena kuti, ‘Mudziwe Yehova,’ chifukwa onse adzandidziwa Ine, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu,” akutero Yehova. “Ndidzawakhululukira zoyipa zawo ndipo sindidzakumbukiranso machimo awo.”
chifundo
pangano
mnzake
Colossians 2:3 — Mwa Iyeyu muli ________ chonse chobisidwa cha nzeru ndi chidziwitso.
chuma
machimo
mafano

← Back to the study