Kodi Baibulo Limati Chiyani Za Nzeru? — Gawo 2 · Malemba a KJV pamodzi ndi Manambala a Strong — Bible Quiz
For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.
This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.
Miyambo 9:10 — Kuopa Yehova ndiye chiyambi cha nzeru; ________ Woyerayo ndiko kukhala womvetsa bwino zinthu.
kudziwa
uchi
tulo
Miyambo 1:7 — Kuopa Yehova ndiye chiyambi cha nzeru. ________ zimanyoza nzeru ndi malangizo.
ochimwa
malamulo
Zitsiru
1 Mafumu 3:9 — Choncho mupatseni mtumiki wanu nzeru zolamulira anthu anu ndi kuti azitha ________ pakati pa chabwino ndi choyipa. Pakuti ndani amene angathe kulamulira anthu anu ochulukawa?”
kusiyanitsa
kuleza mtima
kukula
1 Mafumu 3:12 — Ine ndidzakuchitira zimene wapempha. Ndidzakupatsa mtima wanzeru ndi wozindikira zinthu, kotero kuti sipanakhalepo wina wofanana nawe ndipo sipadzapezekanso wina wonga iwe ________ pako.
anatumiza
mtendere
pambuyo
Miyambo 2:6 — Pakuti Yehova ndiye amapereka nzeru, ndipo mʼkamwa mwake mumachokera ________ ndi kumvetsa zinthu.
mphotho
chidziwitso
zipatso
1 Akorinto 3:19 — Pakuti nzeru ya dziko lapansi ndi yopusa pamaso pa Mulungu. Monga kwalembedwera kuti, “Iye amakola anthu ochenjera mu msampha wa ________ kwawo,”
vumbulutso
kuchenjera
abwenzi
Yakobo 3:15 — “Nzeru” zotere sizochokera kumwamba koma ndi za mʼdziko lapansi, si zauzimu koma ndi za ________.
ziwanda
amasiye
ochimwa
Yakobo 3:17 — Koma nzeru imene imachoka kumwamba, poyamba ndi yangwiro, ndi yokonda ________, yoganizira za ena, yogonjera, yodzaza ndi chifundo ndi chipatso chabwino, yosakondera ndi yoona mtima.
mtendere
ndalama
chimene
1 Akorinto 1:24 — Koma kwa iwo amene Mulungu anawayitana, Ayuda ndi Agriki omwe, Khristu ndi ________ ya Mulungu ndi nzeru za Mulungu.
Mzimu
mphamvu
chiyani
1 Akorinto 1:30 — Nʼchifukwa cha Iye kuti inu muli mwa Khristu Yesu, amene wakhala nzeru ya kwa Mulungu, kwa ife, kunena kuti kulungama kwathu, chiyero ndi ________.
malangizo
mdima
chipulumutso
Akolose 2:3 — Mwa Iyeyu muli ________ chonse chobisidwa cha nzeru ndi chidziwitso.
chuma
machimo
mafano
Miyambo 4:7 — Fundo yayikulu pa za nzeru ndi iyi: upeze nzeru. Kaya ________ china chilichonse chimene ungapeze, koma upeze nzeru yomvetsa bwino zinthu.
pali
yabwino
popanda
Yakobo 3:13 — Ndani mwa inu amene ndi wanzeru ndi womvetsa zinthu? Mulekeni aonetse ndi ________ ake abwino kuti nzeru ndiye zikutsogolera kudzichepetsa kwake ndi zochita zake
makhalidwe
wochimwa
chinyengo
Masalimo 111:10 — Kuopa Yehova ndicho chiyambi cha nzeru; onse amene amatsatira ________ ake amamvetsa bwino zinthu. Iye ndi wotamandika mpaka muyaya.
malangizo
manja
mitima
Mlaliki 4:12 — Munthu mmodzi angathe kugonjetsedwa, koma anthu awiri akhoza kudziteteza. ________ cha maulusi atatu sichidukirapo.
Mlaliki
kuchotsa
Chingwe
Mateyu 12:42 — Mfumu yayikazi yakummwera idzayimirira pa tsiku lachiweruzo ndi ________ uwu ndipo idzawutsutsa pakuti inachokera kumathero a dziko lapansi kudzamva nzeru za Solomoni, ndipo pano pali woposa Solomoni.
mʼbado
mdima
umboni
Link copied
Has this study helped you? Share a short or your full testimony — your story helps someone else find this site.
Save your progress
Optional. You never need an account to use this site.
Keep your quiz scores and your certificate if you change phone or clear your browser.
Restore progress
Restoring replaces the progress on this device, and any certificate you print afterwards will carry the name on the record.
