Aroma 8:15 — Mzimu amene inu munalandira samakusandutsani akapolo, kuti muzikhalanso amantha, koma Mzimu amakusandutsani ana. Ndipo mwa Iye ________ timafuwula kuti, “Abba, Atate.”
Nʼchifukwa
machimo
ife
Machitidwe a Atumwi 8:12 — Koma atakhulupirira ________ akulalikira Uthenga Wabwino wa ufumu wa Mulungu ndiponso dzina la Yesu Khristu, anthuwo anabatizidwa amuna ndi amayi.
Herode
Yesaya
Filipo
Luka 8:15 — Koma mbewu za pa nthaka yabwino zikuyimira anthu amene ali ndi mtima woona ndi wabwino, amene amamva mawu nawasunga, ndipo amalimbikira mpaka amabala ________.
zipatso
thupi
mphamvu
Masalimo 1:2 — Koma chikondwerero chake chili mʼmalamulo a Yehova ndipo mʼmalamulo akewo amalingaliramo ________ ndi usiku.
usana
nsanja
zazimuna
Yoswa 1:8 — Uziwerenga Buku la Malamuloli, uzilingalira zolembedwa mʼmenemo ________ ndi usiku, kuti uchite zonse zimene zinalembedwamo. Ukamatero udzapeza bwino ndi kupambana.
nsanja
usana
zinayi
1 Yohane 1:7 — Koma tikamayenda mʼkuwunika, monga Iye ali mʼkuwunika, pamenepo timayanjana wina ndi mnzake, ndipo magazi a Yesu, Mwana wake, amatitsuka ndi kutichotsera tchimo ________.
lililonse
chinyengo
mlonda
Ahebri 10:24 — Tiziganizira mmene tingalimbikitsirane wina ndi ________ pokondana ndi kuchita ntchito zabwino.
Ahebri 10:38 — Koma ________ wangayo adzakhala ndi moyo mwachikhulupiriro. Ndipo ngati iye abwerera mʼmbuyo chifukwa cha mantha, Ine sindidzakondwera naye.
chisomo
wolungama
chiyembekezo
Luka 14:28 — “Taganizani, ngati wina mwa inu akufuna kumanga ________, kodi iye sayamba wakhala pansi ndi kuganizira za mtengo wake kuti aone ngati ali ndi ndalama zokwanira kuti atsirizire?
nsanja
chigololo
anakumana
Chivumbulutso 12:11 — Choncho, kondwerani, inu dziko lakumwamba ndi onse okhala kumeneko! Koma tsoka dziko lapansi ndi nyanja chifukwa Mdierekezi wagwetsedwa kwa inu! Iye wadzazidwa ndi ________ chifukwa akudziwa kuti nthawi yake ndi yochepa.”
Chivumbulutso 7:9 — Zitatha izi ndinayangʼana patsogolo panga ndipo ndinaona gulu lalikulu la anthu loti munthu sangathe kuliwerenga lochokera dziko lililonse, fuko lililonse, mtundu wa anthu uliwonse ndi chiyankhulo chilichonse, atayima patsogolo pa mpando waufumu, pamaso pa Mwana ________. Iwo anali atavala mikanjo yoyera ndi kunyamula nthambi za kanjedza mʼmanja mwawo.
chisomo
Wankhosa
kumeneko
1 Petro 1:5 — Mwachikhulupiriro, mukusungidwa ndi mphamvu ya Mulungu mpaka ________ chitafika chimene chinakonzedwa kuti adzachionetse nthawi yotsiriza.
manyazi
chilungamo
chipulumutso
Yuda 1:24 — Kwa Iye amene angathe kukusungani kuti mungagwe mʼmachimo, ndiponso amene angathenso kukufikitsani pamaso pake pa ulemerero ________ cholakwa muli okondwa