Kodi Baibulo Limati Chiyani Pankhani ya Kudziletsa (Temperance)? — Gawo 2 · Malemba a KJV pamodzi ndi Manambala a Strong's — Bible Quiz
For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.
This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.
Galatians 5:22 — Koma chipatso cha Mzimu Woyera ndi chikondi, chimwemwe, mtendere, kuleza mtima, chifundo, kukoma mtima, ________
abwenzi
kuuka
kukhulupirika
Proverbs 16:32 — Munthu wosapsa mtima ________ amaposa munthu wankhondo, munthu wowugwira mtima wake amaposa amene amalanda mzinda.
msanga
amayenda
popanda
Proverbs 25:28 — Munthu amene samatha kudziretsa ali ngati mzinda umene adani awuthyola ndi kuwusiya ________ malinga.
ulemerero
mtendere
wopanda
1 Peter 1:13 — Choncho konzani mtima wanu, khalani odziretsa; khazikitsani chiyembekezo chanu kotheratu pa ________ chimene mudzapatsidwe pamene Yesu Khristu adzaonekera.
chisomo
ulemu
Wabwino
1 Peter 5:8 — Khalani odziretsa ndi atcheru. ________ wanu mdierekezi amayendayenda monga mkango wobangula kufunafuna wina kuti amumeze.
mlandu
mtanda
Mdani
1 Thessalonians 5:8 — Koma popeza ndife a usana, tikhale odzisunga, titavala chikhulupiriro ndi chikondi ngati chovala pachifuwa, ndi chiyembekezo cha chipulumutso ngati ________.
mpingo
chipewa
chimwemwe
Romans 6:12 — Nʼchifukwa chake, musalole tchimo lilamulire matupi anu amene anafa kuti mumvere ________ zonyansa.
ochimwa
malonjezo
zilakolako
Daniel 1:8 — Koma Danieli anatsimikiza mtima kuti asadzidetse ndi chakudya ndi vinyo wa mfumu, ndipo anapempha chilolezo kwa mkulu wa ________ za mfumu kuti asadzidetse mwa njira imeneyi.
nduna
masomphenya
zinayi
1 Corinthians 9:25 — Aliyense wochita mpikisano amakonzekera ________. Amachita izi kuti alandire mphotho yankhata yamaluwa yomwe imafota. Koma ife timachita izi kuti tilandire mphotho yosafota.
okondedwa
mwamphamvu
makamaka
Genesis 39:9 — Motero kuti palibe wina ________ kuposa ine mʼnyumba muno. Ndipo palibe chilichonse chimene mbuye wanga sanachipereke kwa ine kupatula inuyo, chifukwa ndinu mkazi wake. Tsono ndingachite bwanji choyipa choterechi ndi kuchimwira Mulungu?”
nkhope
wamkulu
wamngʼono
Genesis 39:12 — Mkazi uja anamugwira mkanjo Yosefe nati, “Tiye ugone nane!” Koma Yosefe anasiya mkanjo wake mʼmanja mwa mkaziyo nathawira ________ kwa nyumba.
masana
kunja
ngamira
Titus 2:12 — Chisomo chimatiphunzitsa kukana moyo osalemekeza Mulungu komanso ________ za dziko lapansi. Ndipo chimatiphunzitsa kukhala moyo odziletsa, olungama ndi opembedza Mulungu nthawi ino
nkhunda
zilakolako
malonjezo
Titus 2:13 — pamene tikudikira chiyembekezo chodala; kuonekera kwa ________ wa Mulungu wathu wamkulu ndi Mpulumutsi, Yesu Khristu
ulemerero
mtendere
wopanda
Link copied
Has this study helped you? Share a short or your full testimony — your story helps someone else find this site.
Save your progress
Optional. You never need an account to use this site.
Keep your quiz scores and your certificate if you change phone or clear your browser.
Restore progress
Restoring replaces the progress on this device, and any certificate you print afterwards will carry the name on the record.
