🌐 Language
'Olelo Hawai'iAfaan Oromoobahasa IndonesiaBelarusianBrezhonegCebuanoChamorroChichewachiShonaChongthuCiyawoDanskDeutschEestiEnglishEspañolEsperantoeʋegbeFrançaisHausaHrvatskiIgboIlocanoItalianoKikuyuKiswahiliKiyombiKreyòl AyisyenLatinaLatviešulietuviųLingálaLugandaMagyarMahasuiMāoriNederlandsNorskPohnpeianPolskiPortuguêsQach’abelRomaniRomânăSanskritSetswanaShqipsrpski jezikSuomiSvenskaTagalogTiếng ViệtTonganTwiTürkçeUyghur tiliYorùbáÍslenskaČeštinaБългарскиРусскийУкраїнськаעבריתاردوالعربيةفارسیكوردی سۆرانیअहिराणी‎नेपालीभद्रवाही‎मराठीमानक हिन्दी‎हरियाणवी‎অসমীয়াবাংলাਪੰਜਾਬੀગુજરાતીଓଡ଼ିଆ‎தமிழ்తెలుగుಕನ್ನಡമലയാളംไทยဗမာἙλληνική中文日本語한국어+ All languages
See More Jesus

Kodi Baibulo Limati Chiyani Pa Za Khama? — Maziko · Malemba a KJV pamodzi ndi Manambala a Strong — Bible Quiz

For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.

This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.

2 Petro 1:5 — Choncho, chitani khama kuwonjezera moyo wabwino pa ________ chanu, ndipo pa moyo wabwino muwonjezerepo nzeru.
chikhulupiriro
chisomo
chuma
Miyambo 12:24 — ________ ntchito mwakhama adzalamulira, koma aulesi adzakhala ngati kapolo.
Mpulumutsi
Ogwira
Myuda
Miyambo 15:19 — Njira ya munthu ________ ndi yowirira ndi mtengo waminga, koma njira ya munthu wolungama ili ngati msewu waukulu.
okongola
waulesi
onyansa
Miyambo 18:9 — Munthu ________ pa ntchito yake ali pachibale ndi munthu amene amawononga zinthu.
mtendere
ulemerero
waulesi
Miyambo 19:24 — Munthu waulesi amapisa dzanja lake mʼmbale; koma sangathe kufikitsa dzanja lakelo ________ pake.
mnzake
mkazi
pakamwa
Miyambo 21:25 — Chilakolako cha munthu ________ chidzamupha yekha chifukwa manja ake amangokhala goba osagwira ntchito.
mtendere
waulesi
wokoma
Miyambo 24:30 — Ndinkayenda mʼmbali mwa munda wa munthu waulesi ndinadutsa munda wamphesa wa munthu wopanda ________.
chuma
chakudya
nzeru
Mlaliki 10:18 — Ngati munthu ndi ________, denga lake limaloshoka; ngati manja ake ndi alobodo nyumba yake imadontha.
kufuwula
waulesi
wokoma
Miyambo 19:15 — Ulesi umagonetsa tulo tofa nato ndipo munthu wosatakataka amakhala ndi ________.
nyale
njala
chikole
Miyambo 6:6 — ________ kwa nyerere, mlesi iwe; kaonetsetse njira zake kuti uphunzirepo kanthu!
dzanja
Pita
kulandira
Miyambo 12:27 — Munthu ________ sapeza chimene akufuna, koma munthu wakhama amapeza chuma chamtengo wapatali.
waulesi
mtendere
ulemerero
Miyambo 13:4 — Munthu ________ amakhumbira zinthu koma sapeza kanthu, koma munthu wakhama adzalemera.
mtendere
waulesi
ulemerero
Miyambo 21:5 — Zolinga za munthu wakhama zimachulukitsa zinthu zake; koma aliyense wochita zinthu ________ amadzakhala wosauka.
nsalu
mwanga
mofulumira
Miyambo 11:27 — Iye amene amafunafuna zabwino mwakhama ________ zabwinozo, koma wofunafuna zoyipa zidzamupeza.
Amasunga
amapeza
amadana
Ahebri 11:6 — Ndipo popanda chikhulupiriro nʼkosatheka kukondweretsa Mulungu, chifukwa aliyense amene amabwera kwa Iye ayenera kukhulupirira kuti Mulungu alipodi ndi kuti Iye amapereka ________ kwa amene akumufunitsitsa.
wosatha
chiyembekezo
mphotho
Machitidwe a Atumwi 18:24 — Pa nthawi yomweyi Myuda wina dzina lake ________, mbadwa ya ku Alekisandriya anafika ku Efeso. Anali munthu wophunzira ndi wodziwa bwino Malemba.
Apolo
Akaya
Korinto
2 Petro 3:14 — Chomwecho okondedwa, popeza inu mukudikira zimenezi, chitani changu kuti mukhale wopanda chilema kuti mukhale pa ________ ndi Iye.
mphamvu
mtendere
Ngakhale
2 Petro 3:10 — Koma tsiku la Ambuye lidzafika ngati ________. Pa tsikuli zinthu zakumwamba zidzachoka ndi phokoso lalikulu. Zinthu zonse zidzawonongedwa ndi moto, ndipo dziko lapansi ndi zonse zili mʼmenemo zidzapsa.
mʼndende
mbala
mthunzi
Ahebri 12:15 — Yangʼanitsitsani kuti wina aliyense asachiphonye chisomo cha Mulungu ndiponso kuti pasaphuke muzu wamkwiyo umene udzabweretsa ________ ndi kudetsa ambiri.
mwambo
chete
mavuto
2 Petro 1:3 — Mulungu mwa ________ zake anatipatsa zonse zofunika kukhala moyo opembedza, potidziwitsa za Iyeyo amene anatiyitana ku ulemerero wake ndi ubwino wake.
chisomo
mphamvu
nyenyezi
1 Petro 2:9 — Koma inu ndinu anthu osankhidwa ndi Mulungu, ansembe achifumu, mtundu woyera mtima, anthu ake enieni a Mulungu, munasankhidwa kuti mulalikire za ntchito zamphamvu za Iye amene anakuyitanani kuti mutuluke mu ________ ndi kulowa mʼkuwunika kwake kodabwitsa.
mdima
ulamuliro
chilungamo
Afilipi 4:8 — ________, abale, muziyika mtima wanu pa zinthu zilizonse zabwino ndi zotamandika monga, zinthu zoona, zinthu zolemekezeka, zinthu zolungama, zinthu zoyera, zinthu zokongola ndi zinthu zosiririka.
makamaka
mwamphamvu
Potsiriza
Afilipi 4:6 — Musade nkhawa ndi kanthu kalikonse, koma pa china chilichonse, mwa ________ ndi chidandaulo pamodzi ndi chiyamiko, perekani zopempha zanu kwa Mulungu.
manyazi
wamphesa
pemphero
Aroma 12:1 — Nʼchifukwa chake ine ndikukupemphani abale, mwa ________ cha Mulungu, kuti mupereke matupi anu monga nsembe yamoyo, yopatulika ndi yokondweretsa Mulungu. Nsembeyi ndiye kupembedza kwanu kwa uzimu.
mwamuna
Atate
chifundo
2 Akorinto 10:3 — Ngakhale ife timakhala mʼdziko lapansi, sitimenya ________ monga mmene dziko lapansi limachitira.
chuma
mtendere
nkhondo
Afilipi 2:5 — Pa ubale wanu wina ndi ________, mukhale ndi mtima wofanana ndi wa Khristu Yesu:
mlandu
mtanda
mnzake
Aroma 8:6 — Kuyika mtima pa zathupi ndi imfa koma kuyika mtima pa za Mzimu ndi moyo ndi ________.
chikondi
mtendere
mphamvu
Yesaya 26:3 — Inu mudzamupatsa munthu wa mtima wokhazikika ________ weniweni.
Mzimu
mtendere
usiku
1 Petro 1:13 — Choncho konzani ________ wanu, khalani odziretsa; khazikitsani chiyembekezo chanu kotheratu pa chisomo chimene mudzapatsidwe pamene Yesu Khristu adzaonekera.
manyazi
mtima
mnzake

← Back to the study