Genesis 3:22 — Ndipo Yehova Mulungu anati, “Tsopano munthu uyu wasanduka mmodzi wa ife, wodziwa zabwino ndi zoyipa. Iyeyu asaloledwe kutambasula dzanja ndi kutengako ________ za mu mtengo wopatsa moyo uja kuti angakhale ndi moyo mpaka muyaya.”
woyamba
zipatso
mlendo
Deuteronomo 30:19 — Lero kumwamba ndi dziko lapansi zikhale mboni zodzakutsutsani pakuti ndayika pamaso panu moyo ndi imfa, ________ ndi matemberero. Tsopano sankhani moyo kuti inu ndi ana anu mukhale ndi moyo.
madalitso
matenda
usana
1 Mafumu 3:9 — Choncho mupatseni mtumiki wanu nzeru zolamulira anthu anu ndi kuti azitha ________ pakati pa chabwino ndi choyipa. Pakuti ndani amene angathe kulamulira anthu anu ochulukawa?”
kusiyanitsa
kuleza mtima
kukula
Yesaya 7:15 — Azidzadya ________ ndi uchi, mpaka atadziwa kukana choyipa ndi kusankha chabwino.
chikhomo
chambiko
matope
Ahebri 5:12 — Ngakhale kuti pa nthawi ino munayenera kukhala aphunzitsi, pakufunikabe munthu wina kuti abwerezenso kudzakuphunzitsani maphunziro oyambira a choonadi cha Mulungu. Ndinu ofunika ________ osati chakudya cholimba!
mkaka
mboni
wosatha
Miyambo 2:3 — ngati upempha kuti uzindikire zinthu inde kupempha ndi mtima wonse kuti ________ womvetsa zinthu
ukhale
chete
ukali
Masalimo 34:14 — Tembenuka kuchoka ku zoyipa ndipo chita zabwino; funafuna ________ ndi kuwulondola.
chakudya
Mantha
mtendere
Miyambo 8:13 — Kuopa Yehova ndiko kudana ndi zoyipa. Ine ndimadana ndi ________, kudzitama, kuchita zoyipa, ndiponso kuyankhula zonyenga.
Mayendedwe
zosungiramo
kunyada
Mateyu 5:16 — Momwemonso kuwunika kwanu kuwale pamaso pa anthu kuti aone ntchito zanu zabwino ndi kulemekeza ________ anu akumwamba.
Atate
Khristu
wantchito
Aroma 2:7 — Iye adzapereka moyo wosatha kwa amene amafunafuna ulemerero, ulemu ndi moyo ________ ntchito zabwino mopirira.
kumvera
pochita
chikondi
Mateyu 19:17 — Yesu anayankha kuti, “Ukundifunsiranji Ine za chinthu chimene ndi chabwino? Pali mmodzi yekha amene ndi wabwino. Ngati ukufuna kulowa mʼmoyo ________ mvera malamulo.”
Uthenga
chigololo
wosatha
Luka 6:45 — Munthu wabwino amatulutsa zinthu zabwino zosungidwa mu mtima mwake, koma munthu oyipa amatulutsa zinthu zoyipa zosungidwa mu mtima mwake. ________ pake pamayankhula zimene zadzaza mu mtima mwake.
pangano
Pakamwa
mnzake
Miyambo 1:33 — Koma aliyense wondimvera adzakhala mwa ________; adzakhala mosatekeseka posaopa chilichonse.”
chilango
bata
wowukira
1 Yohane 5:19 — Tikudziwa kuti ndife ana a Mulungu ndi kuti dziko lonse lapansi lili pansi pa ________ wa woyipayo.
chilango
ulamuliro
umboni
Mateyu 13:19 — Pamene aliyense akumva uthenga wa ufumu koma sawuzindikira, woyipayo amabwera ndi ________ zimene zafesedwa mu mtima mwake. Iyi ndi mbewu yofesedwa mʼmbali mwa njira.
ngongole
kuchotsa
kulikonse
Mateyu 6:22 — “Diso ndi ________ ya thupi. Ngati maso ako ali bwino, thupi lako lonse lidzakhala mʼkuwala.
Aefeso 6:16 — Kuwonjezera pa zonsezi, nyamulani ________ cha chikhulupiriro, ndipo ndi chimenechi mudzatha kuzimitsa mivi yonse yoyaka moto ya oyipayo.
chishango
mtanda
chiphunzitso
1 Yohane 2:14 — Ana okondedwa, ndikukulemberani chifukwa mumawadziwa ________. Abambo, ndikukulemberani chifukwa munamudziwa Iye amene analipo kuyambira pachiyambi. Inu anyamata, ndikukulemberani chifukwa ndinu amphamvu. Mawu a Mulungu amakhala mwa inu ndipo mumamugonjetsa woyipayo.
Atate
mlandu
nyale
Machitidwe a Atumwi 10:38 — kuti Mulungu, anamudzoza Yesu, wa ku ________ ndi Mzimu Woyera ndi mphamvu ndiponso mmene Iye anapita nachita zabwino ndi kuchiritsa onse amene anali pansi pa mphamvu ya mdierekezi, popeza kuti Mulungu anali naye.
Nazareti
Tarisisi
Damasiko
Luka 23:41 — Ife tikulangidwa ________, pakuti ife tikulandira monga mwa ntchito zathu. Koma munthu uyu sanachimwe kanthu.”
Aroma 12:21 — Musagonjetsedwe ndi choyipa, koma gonjetsani choyipa ________ chabwino.
kumvera
chikondi
pochita
1 Yohane 3:8 — Iye amene amachimwa ndi wa ________, chifukwa mdierekezi wakhala akuchimwa kuyambira pa chiyambi. Mwana wa Mulungu anaonekera kuti awononge ntchito za mdierekezi.