🌐 Language
'Olelo Hawai'iAfaan Oromoobahasa IndonesiaBelarusianBrezhonegCebuanoChamorroChichewachiShonaChongthuCiyawoDanskDeutschEestiEnglishEspañolEsperantoeʋegbeFrançaisHausaHrvatskiIgboIlocanoItalianoKikuyuKiswahiliKiyombiKreyòl AyisyenLatinaLatviešulietuviųLingálaLugandaMagyarMahasuiMāoriNederlandsNorskPohnpeianPolskiPortuguêsQach’abelRomaniRomânăSanskritSetswanaShqipsrpski jezikSuomiSvenskaTagalogTiếng ViệtTonganTwiTürkçeUyghur tiliYorùbáÍslenskaČeštinaБългарскиРусскийУкраїнськаעבריתاردوالعربيةفارسیكوردی سۆرانیअहिराणी‎नेपालीभद्रवाही‎मराठीमानक हिन्दी‎हरियाणवी‎অসমীয়াবাংলাਪੰਜਾਬੀગુજરાતીଓଡ଼ିଆ‎தமிழ்తెలుగుಕನ್ನಡമലയാളംไทยဗမာἙλληνική中文日本語한국어+ All languages
See More Jesus

Kodi Baibulo Limati Chiyani Za Zabwino ndi Zoipa? — Gawo 2 · Malemba a KJV ndi Manambala a Strong — Bible Quiz

For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.

This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.

Ahebri 5:14 — Koma chakudya cholimba ndi cha anthu okhwima msinkhu, amene pogwiritsa ntchito nzeru zawo, aphunzira ________ chabwino ndi choyipa.
kusiyanitsa
kupitiriza
utumiki
2 Akorinto 11:3 — Koma ndikuopa kuti monga Hava ananyengedwa ndi ________ kwa njoka, mitima yanunso ingasocheretsedwe kuleka nʼkudzipereka moona mtima ndi modzipereka kwenikweni kwa Khristu.
mayesero
kuchenjera
cholemetsa
Aroma 6:23 — Pakuti ________ a tchimo ndi imfa, koma mphatso yaulere imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha mwa Khristu Yesu Ambuye athu.
malipiro
mdani
Atate
1 Yohane 2:16 — Pakuti zonse za mʼdziko lapansi, ________ za thupi, zinthu zimene maso amakhumbira ndiponso kuyandikira zinthu za moyo uno, zonsezi sizichokera kwa Atate, koma ku dziko lapansi.
ochimwa
kubweretsa
zilakolako
Genesis 3:22 — Ndipo Yehova Mulungu anati, “Tsopano munthu uyu wasanduka mmodzi wa ife, wodziwa zabwino ndi zoyipa. Iyeyu asaloledwe kutambasula dzanja ndi kutengako ________ za mu mtengo wopatsa moyo uja kuti angakhale ndi moyo mpaka muyaya.”
woyamba
zipatso
mlendo
Marko 7:21 — Pakuti kuchokera mʼkati mwa mitima ya anthu, mumatuluka maganizo oyipa, chiwerewere, kuba, kupha, ________
chigololo
mtsikana
dera
Yeremiya 4:22 — Yehova akuti, “Anthu anga ndi ________; iwo sandidziwa. Iwo ndi ana opanda nzeru; samvetsa chilichonse. Ali ndi luso lochita zoyipa, koma sadziwa kuchita zabwino.”
zitsiru
njoka
mikango
Malaki 2:17 — Mwamutopetsa Yehova ndi zoyankhula zanu. Inu mukufunsa kuti, “Kodi tamutopetsa bwanji?” Mwamutopetsa ponena kuti, “Aliyense amene amachita zoyipa ndi wabwino pamaso pa Yehova ndipo iye ________ naye” kapena pofunsa kuti, “Ali kuti Mulungu woweruza mwachilungamo?”
amadalira
chigololo
amakondwera
Yesaya 7:15 — Azidzadya ________ ndi uchi, mpaka atadziwa kukana choyipa ndi kusankha chabwino.
chikhomo
chambiko
matope
Masalimo 97:10 — Iwo amene amakonda Yehova adane ndi zoyipa pakuti Iye amayangʼanira ________ ya amene amamukhulupirira ndipo amawapulumutsa mʼdzanja la anthu oyipa
mʼmabwalo
mabala
miyoyo
1 Mafumu 3:9 — Choncho mupatseni mtumiki wanu nzeru zolamulira anthu anu ndi kuti azitha ________ pakati pa chabwino ndi choyipa. Pakuti ndani amene angathe kulamulira anthu anu ochulukawa?”
kusiyanitsa
kuleza mtima
kukula
Ahebri 5:13 — Aliyense amene amangodya mkaka okha, akanali mwana ________, sakudziwa bwino chiphunzitso cha chilungamo.
wakhanda
chinsalu
mʼkhalapakati
1 Atesalonika 5:22 — ________ choyipa cha mtundu wina uliwonse.
pachiswe
Mupewe
cholemetsa
Aroma 16:19 — Aliyense anamva za ________ kwanu, choncho ndine odzaza ndi chimwemwe chifukwa cha inu. Koma ine ndikufuna kuti inu mukhale anzeru pa zabwino, ndi wopanda cholakwa pa zimene zili zoyipa.
chilango
chikondi
kumvera
Machitidwe a Atumwi 10:38 — kuti Mulungu, anamudzoza Yesu, wa ku ________ ndi Mzimu Woyera ndi mphamvu ndiponso mmene Iye anapita nachita zabwino ndi kuchiritsa onse amene anali pansi pa mphamvu ya mdierekezi, popeza kuti Mulungu anali naye.
Nazareti
Tarisisi
Damasiko
1 Petro 3:11 — Apewe zoyipa, ndipo azichita zabwino. Afunefune ________ ndi kuyesetsa kuwupeza.
chikondi
mtendere
Mzimu
Aroma 12:21 — Musagonjetsedwe ndi choyipa, koma gonjetsani choyipa ________ chabwino.
kumvera
chilango
pochita
Masalimo 34:14 — Tembenuka kuchoka ku zoyipa ndipo chita zabwino; funafuna ________ ndi kuwulondola.
chakudya
mphamvu
mtendere
Aroma 12:9 — Chikondi chikhale chopanda ________. Dana nacho choyipa; gwiritsitsa chabwino.
chinyengo
lililonse
mwadzidzidzi
Genesis 3:13 — Tsono Yehova Mulungu anati kwa mkaziyo, “Wachitachi nʼchiyani?” Mkaziyo anati, “________ inandinamiza, ndipo ndinadya.”
mkaka
Njoka
kasupe
Aroma 5:19 — Pakuti kusamvera kwa munthu mmodzi kunasandutsa anthu ambiri kukhala ________, chimodzimodzinso anthu ambiri adzasanduka olungama kudzera mwa munthu mmodzinso.
zilakolako
ochimwa
ziwanda
1 Petro 2:24 — Iye mwini anasenza machimo athu mʼthupi lake pa mtanda, kuti ife tife kutchimo ndi kukhala ndi moyo potsata chilungamo, ndipo ndi ________ ake munachiritsidwa.
miliri
mabala
mapemphero
Chivumbulutso 2:7 — Amene ali ndi makutu, amve zimene Mzimu akuwuza mipingo. Amene adzapambana, ndidzamupatsa ufulu wakudya ________ za mtengo wopatsa moyo umene uli ku paradizo wa Mulungu.
chikondi
yekha
zipatso
Chivumbulutso 22:2 — Ukuyenda pakati pa msewu waukulu wa mu mzindawo. Mbali iliyonse ya mtsinjewo kunali mtengo wamoyo, utabala zipatso khumi ndi ziwiri. Kubereka zipatso mwezi uliwonse. Ndipo masamba a mtengowo ndi ________ wochiritsa anthu a mitundu ina.
chilumba
mankhwala
galasi

← Back to the study