🌐 Language
'Olelo Hawai'iAfaan Oromoobahasa IndonesiaBelarusianBrezhonegCebuanoChamorroChichewachiShonaChongthuCiyawoDanskDeutschEestiEnglishEspañolEsperantoeʋegbeFrançaisHausaHrvatskiIgboIlocanoItalianoKikuyuKiswahiliKiyombiKreyòl AyisyenLatinaLatviešulietuviųLingálaLugandaMagyarMahasuiMāoriNederlandsNorskPohnpeianPolskiPortuguêsQach’abelRomaniRomânăSanskritSetswanaShqipsrpski jezikSuomiSvenskaTagalogTiếng ViệtTonganTwiTürkçeUyghur tiliYorùbáÍslenskaČeštinaБългарскиРусскийУкраїнськаעבריתاردوالعربيةفارسیكوردی سۆرانیअहिराणी‎नेपालीभद्रवाही‎मराठीमानक हिन्दी‎हरियाणवी‎অসমীয়াবাংলাਪੰਜਾਬੀગુજરાતીଓଡ଼ିଆ‎தமிழ்తెలుగుಕನ್ನಡമലയാളംไทยဗမာἙλληνική中文日本語한국어+ All languages
See More Jesus

Baibulo Limati Chiyani Za Chifundo? — Maziko · Malemba a KJV Ndi Manambala a Strong's — Bible Quiz

For each reference below, choose what that verse teaches. Your score appears at the end.

This is the graded quiz. Pass it to earn credit toward your Ministry Certificate of Endorsement.

Mateyu 9:13 — Koma pitani kaphunzireni tanthauzo la mawu awa: ‘Ndimafuna chifundo osati nsembe ayi.’ Pakuti sindinabwere kudzayitana olungama koma ________.”
malemba
mizimu
ochimwa
Luka 10:37 — Katswiri wa Malamulo uja anayankha kuti, “Amene anamuchitira ________.” Yesu anamuwuza kuti, “Pita, uzikachita chimodzimodzi.”
Atate
mbuye
chifundo
Mateyu 18:33 — Kodi iwe sukanamuchitira chifundo ________ mnzako monga momwe ine ndinakuchitira iwe?’
Khristu
Atate
wantchito
1 Petro 1:3 — Alemekezedwe Mulungu, ________ wa Ambuye athu Yesu Khristu. Mwachifundo chake chachikulu anatibadwitsa kwatsopano, mʼchiyembekezo chamoyo pomuukitsa Yesu Khristu kwa akufa
mlandu
makolo
Atate
Ahebri 2:17 — Chifukwa cha zimenezi, Iye anayenera kukhala wofanana ndi abale ake pa zonse, kuti akhale mkulu wa ansembe wachifundo ndi wokhulupirika potumikira Mulungu, kuti potero achotse ________ a anthu.
mawu
mphamvu
machimo
Marko 10:47 — Pamene anamva kuti anali Yesu wa ku ________, anayamba kufuwula kuti, “Yesu, Mwana wa Davide, mundichitire chifundo!”
Andreya
Nazareti
Sidoni
Machitidwe a Atumwi 9:36 — Ku ________ kunali wophunzira wina dzina lake Tabita (mʼChigriki amati Dorika) amene nthawi zonse ankachita zachifundo ndiponso kuthandiza osauka.
Nazareti
Yudeya
Yopa
Genesis 19:29 — Choncho Mulungu anawononga mizinda ya ku ________, koma anakumbukira pemphero la Abrahamu natulutsa Loti ku sulufule ndi moto zimene zinawononga mizinda ya kumene Loti amakhalako.
chigwa
mmawa
dzuwa
Genesis 32:10 — Ine siwoyenera kulandira kukoma mtima kwanu ndi ________ kwanu kumene mwaonetsa wantchito wanu. Ndinali ndi ndodo yokha pamene ndinawoloka Yorodani uyu koma tsopano ndili ndi magulu awiri.
malangizo
chanu
kukhulupirika
Masalimo 136:1 — Yamikani Yehova chifukwa ndi wabwino. Pakuti chikondi chake chosasinthika ________.
amakondwera
nʼchamuyaya
amadalira
Masalimo 136:4 — Iye yekhayo amene amachita ________ zazikulu, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.
mantha
ndithudi
zodabwitsa
Masalimo 136:23 — Amene anatikumbukira ife anthu opeputsidwa, pakuti chikondi chake chosasinthika ________.
amakondwera
amachita
nʼchamuyaya
Masalimo 136:26 — Yamikani Mulungu wakumwamba, pakuti chikondi chake chosasinthika ________.
amakondwera
nʼchamuyaya
amachita

← Back to the study