KALE UNAYIKA MAYAMBIRIRO A DZIKO LAPANSI --> INU NDINU OMWEWO, NDIPO ZAKA ZANU SIZIDZATHA.
Mpando wanu waufumu, Inu Mulungu --> choncho Mulungu, Mulungu wanu, wakukhazikani pamwamba pa anzanu pokudzozani ndi mafuta a chimwemwe.
MASALIMO 110:1
Aliyense wokhulupirira Mwanayo ali ndi moyo wosatha.
MABUKU ANATSEGULIDWA + BUKU LINA LINATSEGULIDWANSO, LIMENE NDI BUKU LA MOYO --> ALIYENSE AMENE SANAPEZEKE WOLEMBEDWA MU BUKU LA MOYO ANAPONYEDWA MU NYANJA YA MOTO.
YEHOVA ANATI KWA AMBUYE ANGA, KHALA PANSI KUMANJA KWANGA --> MPAKA NDIDZASANDUTSE ADANI AKO KUKHALA CHOPONDAPO MAPAZI AKO.
MATEYU 22:41
WOPANGIDWA MWA MBEU YA DAVIDI MOGWIRIZANA NDI THUPI --> WOTSIMIKIZIKA KUKHALA MWANA WA MULUNGU MWA MPHAMVU, MWA KUUKA KWAKE KWA AKUFA.
NDINAPEREKA MSANA WANGA KWA OWOMBA --> SINDINABISE NKHOPE YANGA KU MANYAZI NDI MATE.
Ngati Davide amutcha Ambuye, nanga ndi Mwana wake bwanji? --> Ndipo panalibe munthu amene anatha kumuyankha mawu.
MACHITIDWE A ATUMWI 2:32
Aliyense wokhulupirira Mwanayo ali ndi moyo wosatha.
DAVIDE SANAKWERE KUMWAMBA --> MULUNGU WAMUPANGA YESU UJA, AMENE INU MUNAMPACHIKA, KUKHALA AMBUYE NDI KHRISTU.
KHRISTU WAUKA KWA AKUFA, NDIPO WAKHALA ZIPATSO ZOYAMBA ZA IWO AMENE ANAGONA.
MASALIMO 110:4
KULIBE CHIYAMBI CHA MASIKU, KAPENA MAPETO A MOYO --> AMAKHALABE WANSEMBE MUYAYA.
Yehova walumbira ndipo sadzasintha maganizo ake --> Ndiwe wansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melikizedeki.
Nʼchifukwa chake Khristu sanadzipatse yekha ulemu wokhala Mkulu wa ansembe --> Iwe ndiwe wansembe mpaka muyaya, monga mwa unsembe wa Melikizedeki.
AHEBRI 5:5
KULIBE CHIYAMBI CHA MASIKU, KAPENA MAPETO A MOYO --> AMAKHALABE WANSEMBE MUYAYA.
IYE AKHALAPO MUYAYA + ALI NDI UNSEMBE WOSASINTHA --> IYE AKHOZA KUPULUMUTSA KWATHUNTHU.

AHEBRI 7:3
KULIBE CHIYAMBI CHA MASIKU, KAPENA MAPETO A MOYO --> AMAKHALABE WANSEMBE MUYAYA.
Yehova walumbira ndipo sadzasintha maganizo ake --> Ndiwe wansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melikizedeki.
IYE AKHALAPO MUYAYA + ALI NDI UNSEMBE WOSASINTHA --> IYE AKHOZA KUPULUMUTSA KWATHUNTHU.
AHEBRI 7:24

AMENE ANAKHALA PA KAVALOYO ANATCHEDWA WOKHULUPIRIKA NDI WOONA --> DZINA LAKE LITCHEDWA MAWU A MULUNGU.
M'MOTO WA LAWI, KUBWEZERA WOBWEZERA IWO AMENE SADZIWA MULUNGU, NDI IWO AMENE SAMVERA UTHENGA WABWINO --> PAMENE ADZABWERA KUTI ALEMEKEZEKE MWA OYERA MTIMA AKE.
CHIVUMBULUTSO 19:16
MFUMU YA MAFUMU NDI MBUYE WA AMBUYE.
Yesu amene wachotsedwa pakati panu ndi kupita kumwamba, adzabweranso mʼnjira yomweyi mwamuona akupita kumwamba.
AMENE ANAKHALA PA KAVALOYO ANATCHEDWA WOKHULUPIRIKA NDI WOONA --> DZINA LAKE LITCHEDWA MAWU A MULUNGU.
CHIVUMBULUTSO 20:11
Koma zoyipa zanu zakulekanitsani ndi Mulungu wanu.
MFUMU YA MAFUMU NDI MBUYE WA AMBUYE.
MABUKU ANATSEGULIDWA + BUKU LINA LINATSEGULIDWANSO, LIMENE NDI BUKU LA MOYO --> ALIYENSE AMENE SANAPEZEKE WOLEMBEDWA MU BUKU LA MOYO ANAPONYEDWA MU NYANJA YA MOTO.
YOHANE 3:18
Chipulumutso sichipezeka mwa wina aliyense --> pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo limene lapatsidwa kwa anthu limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.
IYE AMENE SAKHULUPIRIRA WAWERUZIDWA KALE.
Aliyense wokhulupirira Mwanayo ali ndi moyo wosatha.
YOHANE 3:36
Aliyense wokhulupirira Mwanayo ali ndi moyo wosatha.
IYE AMENE SAKHULUPIRIRA WAWERUZIDWA KALE.
Pakuti malipiro a tchimo ndi imfa --> koma mphatso yaulere imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha mwa Khristu Yesu Ambuye athu.
AROMA 6:23
Chipulumutso sichipezeka mwa wina aliyense --> pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo limene lapatsidwa kwa anthu limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.
Mzimu Woyera ndi mkwatibwi akuti, “Bwerani --> ndipo aliyense amene afuna alandire mphatso yaulere ya madzi amoyo.

MACHITIDWE A ATUMWI 4:12
Chipulumutso sichipezeka mwa wina aliyense --> pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo limene lapatsidwa kwa anthu limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.
Mzimu Woyera ndi mkwatibwi akuti, “Bwerani --> ndipo aliyense amene afuna alandire mphatso yaulere ya madzi amoyo.
IYE AMENE SAKHULUPIRIRA WAWERUZIDWA KALE.
CHIVUMBULUTSO 22:17
Aliyense wokhulupirira Mwanayo ali ndi moyo wosatha.
Chipulumutso sichipezeka mwa wina aliyense --> pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo limene lapatsidwa kwa anthu limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.
Mzimu Woyera ndi mkwatibwi akuti, “Bwerani --> ndipo aliyense amene afuna alandire mphatso yaulere ya madzi amoyo.
YOHANE 3:17
Aliyense wokhulupirira Mwanayo ali ndi moyo wosatha.
Pakuti Mulungu sanatume Mwana wake ku dziko lapansi --> koma kuti akapulumutse dziko lapansi.
Chipulumutso sichipezeka mwa wina aliyense --> pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo limene lapatsidwa kwa anthu limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.
MACHITIDWE A ATUMWI 17:26
IYE AMENE SAKHULUPIRIRA WAWERUZIDWA KALE.
WAPANGA MTUNDU UMODZI WA ANTHU ONSE KUCHOKERA M'MAGAZI AMODZI --> KUTI AFUNAFUNE AMBUYE, NDI KUMPEZA + IYE SALI KUTALI NA MMODZI ALIYENSE WA ATHU.